-
Esitere 4:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 “Atumiki onse a mfumu ndi anthu a m’zigawo za mfumu akudziwa kuti mfumu ili ndi lamulo limodzi lokhudza mwamuna kapena mkazi aliyense wokaonekera kwa iye m’bwalo lamkati+ asanaitanidwe. Lamuloli+ ndi lakuti aphedwe. Koma ngati mfumu yamuloza ndi ndodo yachifumu ya golide, pamenepo adzakhala ndi moyo.+ Ndiye ine sindinaitanidwe kukaonekera kwa mfumu kwa masiku 30 tsopano.”
-