Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndiyeno mfumu inakonda kwambiri Esitere kuposa akazi ena onse, moti mfumu inakondwera naye ndipo inamusonyeza kukoma mtima kosatha kuposa anamwali ena onse.+ Pamenepo mfumu inamuveka duku lachifumu kumutu kwake ndi kumusandutsa mfumukazi+ m’malo mwa Vasiti.

  • Esitere 8:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno Moredekai anachoka pamaso pa mfumu atavala chovala chachifumu+ cha buluu ndi nsalu yoyera. Analinso atavala chisoti chachikulu chachifumu chagolide, mkanjo wa nsalu yabwino kwambiri yaubweya wa nkhosa+ wonyika mu utoto wofiirira.+ Ndipo mumzinda wa Susani munamveka kufuula kwa chisangalalo ndi kukondwera.+

  • Mateyu 11:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Nanga munapita kukaona chiyani? Munthu wovala zovala zapamwamba kapena? Iyayi, pajatu ovala zovala zapamwamba amapezeka m’nyumba za mafumu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena