14 Pakuti ngati iwe ukhala chete pa nthawi ino, thandizo ndi chipulumutso cha Ayuda zidzachokera kwina.+ Koma anthu inu, iwe ndi nyumba ya bambo ako, nonse mudzatheratu. Ndipo ndani akudziwa? Mwina iwe wakhala mfumukazi kuti uthandize pa nthawi ngati imeneyi.”+