-
Esitere 2:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Tsopano Hegai anasangalala naye mtsikanayu moti anam’sonyeza kukoma mtima kosatha.+ Mwamsanga anam’paka mafuta okongoletsa,+ anam’patsa chakudya chapadera ndiponso anam’patsa atsikana 7 osankhidwa kuchokera kunyumba ya mfumu. Kenako anam’samutsa pamodzi ndi atsikanawo n’kuwapatsa malo abwino kwambiri m’nyumba ya akaziyo.
-