Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 11:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Munthu wosonyeza kukoma mtima kosatha amapindulitsa moyo wake,+ koma munthu wankhanza amachititsa kuti thupi lake linyanyalidwe.+

  • Miyambo 14:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Anthu okonza chiwembu amasochera,+ koma anthu okonzekera kuchita zabwino amapeza kukoma mtima kosatha ndi choonadi.+

  • Miyambo 16:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova akasangalala ndi njira za munthu,+ amachititsa ngakhale adani a munthuyo kukhala naye pa mtendere.+

  • Miyambo 19:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Chinthu chosiririka mwa munthu wochokera kufumbi ndicho kukoma mtima kwake kosatha,+ ndipo munthu wosauka ali bwino kuposa munthu wonama.+

  • Danieli 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chotero Mulungu woona anachititsa kuti mkulu wa nduna za panyumba ya mfumu asonyeze Danieli kukoma mtima kosatha ndi chifundo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena