1 Mafumu 8:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mukhululukire+ anthu anu amene anakuchimwirani.+ Muwakhululukirenso chifukwa cha malamulo anu onse amene anaphwanya,+ komanso owagwirawo akamawaona azikhudzidwa mtima+ ndi kuwachitira chisoni, Salimo 106:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo anali kuchititsa kuti anthu onse owagwira ukapoloAwamvere chisoni.+ Miyambo 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova akasangalala ndi njira za munthu,+ amachititsa ngakhale adani a munthuyo kukhala naye pa mtendere.+
50 Mukhululukire+ anthu anu amene anakuchimwirani.+ Muwakhululukirenso chifukwa cha malamulo anu onse amene anaphwanya,+ komanso owagwirawo akamawaona azikhudzidwa mtima+ ndi kuwachitira chisoni,
7 Yehova akasangalala ndi njira za munthu,+ amachititsa ngakhale adani a munthuyo kukhala naye pa mtendere.+