Miyambo 31:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chikoka chikhoza kukhala chachinyengo+ ndipo kukongola kukhoza kukhala kopanda phindu,+ koma mkazi woopa Yehova ndi amene amatamandidwa chifukwa cha zochita zake.+
30 Chikoka chikhoza kukhala chachinyengo+ ndipo kukongola kukhoza kukhala kopanda phindu,+ koma mkazi woopa Yehova ndi amene amatamandidwa chifukwa cha zochita zake.+