Esitere 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pambuyo pake, Mfumu Ahasiwero analemekeza Hamani+ mwana wa Hamedata Mwagagi,+ ndipo anam’kweza+ ndi kum’patsa mpando wapamwamba kuposa akalonga ena onse amene mfumuyo inali nawo.+ Esitere 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Hamani anapitiriza kunena kuti: “Kuwonjezera apo, Mfumukazi Esitere sanaitane wina aliyense kuphwando limene anakonza, koma anaitana ine ndi mfumu,+ ndipo mawa+ wandiitananso pamodzi ndi mfumu.
3 Pambuyo pake, Mfumu Ahasiwero analemekeza Hamani+ mwana wa Hamedata Mwagagi,+ ndipo anam’kweza+ ndi kum’patsa mpando wapamwamba kuposa akalonga ena onse amene mfumuyo inali nawo.+
12 Pamenepo Hamani anapitiriza kunena kuti: “Kuwonjezera apo, Mfumukazi Esitere sanaitane wina aliyense kuphwando limene anakonza, koma anaitana ine ndi mfumu,+ ndipo mawa+ wandiitananso pamodzi ndi mfumu.