Esitere 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 m’masiku amenewo mfumuyo inali kulamulira ili m’nyumba yachifumu+ yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri+ ya ku Susani.+ Danieli 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nditayamba kuona masomphenyawo ndinapezeka kuti ndili kunyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani,+ imene ili m’chigawo cha Elamu.+ M’masomphenyawo ndinapezeka kuti ndili m’mphepete mwa mtsinje wa Ulai.+
2 m’masiku amenewo mfumuyo inali kulamulira ili m’nyumba yachifumu+ yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri+ ya ku Susani.+
2 Nditayamba kuona masomphenyawo ndinapezeka kuti ndili kunyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani,+ imene ili m’chigawo cha Elamu.+ M’masomphenyawo ndinapezeka kuti ndili m’mphepete mwa mtsinje wa Ulai.+