Danieli 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano inu mfumu khazikitsani lamulo ndipo musaine+ kuti lamulolo lisasinthe, mogwirizana ndi malamulo a Amedi ndi Aperisiya,+ amene sasintha.”+ Danieli 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamapeto pake, amuna amphamvu amenewa anapita kwa mfumu ali chigulu ndipo anaiuza kuti: “Inu mfumu, mukudziwa kuti malamulo a Amedi ndi Aperisiya amanena kuti lamulo lililonse+ lokhazikitsidwa ndi mfumu siliyenera kusinthidwa.”+
8 Tsopano inu mfumu khazikitsani lamulo ndipo musaine+ kuti lamulolo lisasinthe, mogwirizana ndi malamulo a Amedi ndi Aperisiya,+ amene sasintha.”+
15 Pamapeto pake, amuna amphamvu amenewa anapita kwa mfumu ali chigulu ndipo anaiuza kuti: “Inu mfumu, mukudziwa kuti malamulo a Amedi ndi Aperisiya amanena kuti lamulo lililonse+ lokhazikitsidwa ndi mfumu siliyenera kusinthidwa.”+