Ekisodo 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo Mose anatambasula dzanja lake ndi kuloza kumwamba ndi ndodo yake. Atatero, Yehova anachititsa mabingu ndipo anagwetsa matalala+ ndi moto padziko lapansi. Choncho Yehova anapitiriza kugwetsa matalala padziko la Iguputo. 1 Samueli 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Samueli anafuulira Yehova,+ moti Yehova anadzetsa mabingu ndi mvula tsiku limenelo.+ Pamenepo anthu onse anachita mantha kwambiri ndi Yehova ndiponso ndi Samueli. Yobu 36:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndi zimenezi, iye amaweruza mokomera mitundu ya anthu.+Amapereka chakudya chochuluka.+
23 Ndipo Mose anatambasula dzanja lake ndi kuloza kumwamba ndi ndodo yake. Atatero, Yehova anachititsa mabingu ndipo anagwetsa matalala+ ndi moto padziko lapansi. Choncho Yehova anapitiriza kugwetsa matalala padziko la Iguputo.
18 Choncho Samueli anafuulira Yehova,+ moti Yehova anadzetsa mabingu ndi mvula tsiku limenelo.+ Pamenepo anthu onse anachita mantha kwambiri ndi Yehova ndiponso ndi Samueli.