Yobu 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Monga mbidzi+ m’chipululu,Osaukawo amapita kukafunafuna chakudya.Chipululu chimapatsa aliyense chakudya cha ana ake. Yeremiya 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mbidzi+ zangoima chilili m’mapiri opanda kanthu. Zikupuma mwawefuwefu ngati mimbulu. Maso awo achita mdima chifukwa kulibe msipu.+
5 Monga mbidzi+ m’chipululu,Osaukawo amapita kukafunafuna chakudya.Chipululu chimapatsa aliyense chakudya cha ana ake.
6 Mbidzi+ zangoima chilili m’mapiri opanda kanthu. Zikupuma mwawefuwefu ngati mimbulu. Maso awo achita mdima chifukwa kulibe msipu.+