Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 29:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Adzanena mawuwo akadzaonanso sulufule, mchere+ ndi kutentha,+ moti m’dzikomo simungabzalidwe mbewu, simungaphuke kalikonse ndipo simungamere chomera chilichonse, mofanana ndi Sodomu ndi Gomora,+ Adima+ ndi Zeboyimu,+ mizinda imene Yehova anaiwononga mu ukali ndi mkwiyo wake.+

  • Yesaya 42:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndidzawononga+ mapiri ndi zitunda. Ndidzaumitsa zinthu zonse zimene zinamera mmenemo. Mitsinje ndidzaisandutsa zilumba ndipo madambo ndidzawaumitsa.+

  • Yeremiya 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kodi dzikoli lifotabe mpaka liti?+ Kodi zomera za m’minda yonse ziumabe mpaka liti?+ Chifukwa chakuti anthu a m’dzikoli ndi oipa, zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka zinachoka.+ Pakuti anthuwo akuti: “Iye sakuona zimene zidzatichitikira m’tsogolo.”

  • Yoweli 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ziweto zausa moyo. Gulu la ng’ombe likuyendayenda mosokonezeka pakuti kulibe msipu woti zidye.+ Ndiponso gulu la nkhosa ndi limene lalangidwa chifukwa cha uchimo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena