Salimo 104:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akasupewo amapereka madzi kwa zilombo zonse zakutchire.+Nthawi zonse mbidzi+ zimapha ludzu lawo mmenemo. Yeremiya 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mbidzi+ zangoima chilili m’mapiri opanda kanthu. Zikupuma mwawefuwefu ngati mimbulu. Maso awo achita mdima chifukwa kulibe msipu.+ Yesaya 32:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti nsanja yokhalamo yasiyidwa,+ piringupiringu amene anali mumzindamo watha. Ofeli+ ndi nsanja ya mlonda zasanduka tchire. Mpaka kalekale zidzakhala malo osangalalako mbidzi, ndi odyetserako ziweto,
11 Akasupewo amapereka madzi kwa zilombo zonse zakutchire.+Nthawi zonse mbidzi+ zimapha ludzu lawo mmenemo.
6 Mbidzi+ zangoima chilili m’mapiri opanda kanthu. Zikupuma mwawefuwefu ngati mimbulu. Maso awo achita mdima chifukwa kulibe msipu.+
14 Pakuti nsanja yokhalamo yasiyidwa,+ piringupiringu amene anali mumzindamo watha. Ofeli+ ndi nsanja ya mlonda zasanduka tchire. Mpaka kalekale zidzakhala malo osangalalako mbidzi, ndi odyetserako ziweto,