Genesis 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako, Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kufumbi lapansi,+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ m’mphuno mwake, munthuyo n’kukhala wamoyo.+ Yesaya 45:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsoka kwa amene walimbana ndi amene anamuumba,+ ngati phale limene likulimbana ndi mapale ena amene ali pansi. Kodi dongo+ lingafunse amene akuliumba kuti: “Kodi ukupanga chiyani?” Ndipo kodi chimene unapanga chinganene kuti: “Amene uja alibe manja”? Aroma 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kodi simudziwa kuti woumba mbiya+ ali ndi ufulu woumba chiwiya china cholemekezeka, china chonyozeka kuchokera pa dongo limodzi?+
7 Kenako, Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kufumbi lapansi,+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ m’mphuno mwake, munthuyo n’kukhala wamoyo.+
9 Tsoka kwa amene walimbana ndi amene anamuumba,+ ngati phale limene likulimbana ndi mapale ena amene ali pansi. Kodi dongo+ lingafunse amene akuliumba kuti: “Kodi ukupanga chiyani?” Ndipo kodi chimene unapanga chinganene kuti: “Amene uja alibe manja”?
21 Kodi simudziwa kuti woumba mbiya+ ali ndi ufulu woumba chiwiya china cholemekezeka, china chonyozeka kuchokera pa dongo limodzi?+