Deuteronomo 32:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mtengo wawo wa mpesa ndi wochokera ku mtengo wa mpesa wa ku Sodomu,Ndi kuminda ya m’mapiri a ku Gomora.+ Zipatso zawo za mphesa ndi zakupha,Ndipo ndi zowawa.+ Rute 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma iye powayankha anali kunena kuti: “Musanditchulenso kuti Naomi,* muzinditchula kuti Mara,* chifukwa Wamphamvuyonse+ wachititsa moyo wanga kukhala wowawa kwambiri.+ Yobu 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mkwiyo wa Mulungu wandikhadzula. Iye ali nane chidani+Ndipo akundikukutira mano.+Mdani wanga akundiyang’ana ndi diso lozonda.+ Yobu 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mkwiyo wake nawonso wandiyakira,+Ndipo akungondiona ngati ndine mdani wake. Yobu 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu amapeza ponditsutsira,Amanditenga ngati mdani wake.+
32 Mtengo wawo wa mpesa ndi wochokera ku mtengo wa mpesa wa ku Sodomu,Ndi kuminda ya m’mapiri a ku Gomora.+ Zipatso zawo za mphesa ndi zakupha,Ndipo ndi zowawa.+
20 Koma iye powayankha anali kunena kuti: “Musanditchulenso kuti Naomi,* muzinditchula kuti Mara,* chifukwa Wamphamvuyonse+ wachititsa moyo wanga kukhala wowawa kwambiri.+
9 Mkwiyo wa Mulungu wandikhadzula. Iye ali nane chidani+Ndipo akundikukutira mano.+Mdani wanga akundiyang’ana ndi diso lozonda.+