Yobu 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Masiku anga akufulumira+ kuposa mmene chimathamangira chowombera nsalu,Iwo afika pamapeto popanda chiyembekezo.+ Yobu 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Komanso masiku anga akufulumira kwambiri kuposa munthu wothamanga.+Iwo athawa ndipo ndithu sadzaona zabwino. Yesaya 38:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine ndinati: “Pakatikati pa masiku anga ndidzalowa pazipata+ za Manda.Ndidzamanidwa zaka zanga zotsala.”+
6 Masiku anga akufulumira+ kuposa mmene chimathamangira chowombera nsalu,Iwo afika pamapeto popanda chiyembekezo.+
25 Komanso masiku anga akufulumira kwambiri kuposa munthu wothamanga.+Iwo athawa ndipo ndithu sadzaona zabwino.
10 Ine ndinati: “Pakatikati pa masiku anga ndidzalowa pazipata+ za Manda.Ndidzamanidwa zaka zanga zotsala.”+