1 Samueli 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho munthu wobweretsa uthengayo anayankha kuti: “Aisiraeli athawa pamaso pa Afilisiti, ndipo agonjetsedwa koopsa.+ Ana anunso awiri, Hofeni ndi Pinihasi,+ aphedwa. Ngakhalenso likasa la Mulungu woona lalandidwa.”+ Danieli 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Usiku womwewo, Belisazara mfumu ya Akasidi anaphedwa,+
17 Choncho munthu wobweretsa uthengayo anayankha kuti: “Aisiraeli athawa pamaso pa Afilisiti, ndipo agonjetsedwa koopsa.+ Ana anunso awiri, Hofeni ndi Pinihasi,+ aphedwa. Ngakhalenso likasa la Mulungu woona lalandidwa.”+