Yobu 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Ineyo ndikunyansidwa ndi moyo wanga.+Ndilankhula mwamphamvu za nkhawa zanga.Ndilankhula chifukwa cha kuwawa kwa moyo wanga. Yobu 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dziwani kuti Mulungu mwiniwakeyo ndi amene wandisocheretsa,Ndipo wandizunguliza ndi ukonde wake wosakira nyama.+
10 “Ineyo ndikunyansidwa ndi moyo wanga.+Ndilankhula mwamphamvu za nkhawa zanga.Ndilankhula chifukwa cha kuwawa kwa moyo wanga.
6 Dziwani kuti Mulungu mwiniwakeyo ndi amene wandisocheretsa,Ndipo wandizunguliza ndi ukonde wake wosakira nyama.+