Yobu 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi Wamphamvuyonse ndani kuti tim’tumikire?+Ndipo kulankhula naye kungatipindulitse chiyani?’+ Yobu 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa wanena kuti, ‘Mwamuna wamphamvu sapindula kanthu+Akamachita zosangalatsa Mulungu.’