Yobu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 N’chifukwa chake ndikunena kuti zonsezo mfundo yake ndi imodzi, yakuti:‘Iye amapha osalakwa komanso oipa.’+ Yobu 35:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwanena kuti, ‘Kodi kulungamako n’kwantchito yanji kwa inu?+Kodi kundipindulitsa chiyani kuposa chimene ndikanapindula pochimwa?’+ Malaki 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Inu mwanena kuti, ‘Kutumikira Mulungu n’kopanda phindu.+ Tapindulanji chifukwa chomutumikira ndiponso chifukwa choyenda mwachisoni pamaso pa Yehova wa makamu?+
22 N’chifukwa chake ndikunena kuti zonsezo mfundo yake ndi imodzi, yakuti:‘Iye amapha osalakwa komanso oipa.’+
3 Mwanena kuti, ‘Kodi kulungamako n’kwantchito yanji kwa inu?+Kodi kundipindulitsa chiyani kuposa chimene ndikanapindula pochimwa?’+
14 “Inu mwanena kuti, ‘Kutumikira Mulungu n’kopanda phindu.+ Tapindulanji chifukwa chomutumikira ndiponso chifukwa choyenda mwachisoni pamaso pa Yehova wa makamu?+