Yobu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 N’chifukwa chake ndikunena kuti zonsezo mfundo yake ndi imodzi, yakuti:‘Iye amapha osalakwa komanso oipa.’+ Salimo 73:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndithudi, ndayeretsa mtima wanga pachabe,+Ndipo ndasamba m’manja mwanga pachabe posonyeza kuti ndine wopanda cholakwa.+ Malaki 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Inu mwanena kuti, ‘Kutumikira Mulungu n’kopanda phindu.+ Tapindulanji chifukwa chomutumikira ndiponso chifukwa choyenda mwachisoni pamaso pa Yehova wa makamu?+
22 N’chifukwa chake ndikunena kuti zonsezo mfundo yake ndi imodzi, yakuti:‘Iye amapha osalakwa komanso oipa.’+
13 Ndithudi, ndayeretsa mtima wanga pachabe,+Ndipo ndasamba m’manja mwanga pachabe posonyeza kuti ndine wopanda cholakwa.+
14 “Inu mwanena kuti, ‘Kutumikira Mulungu n’kopanda phindu.+ Tapindulanji chifukwa chomutumikira ndiponso chifukwa choyenda mwachisoni pamaso pa Yehova wa makamu?+