Salimo 48:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Mumzinda wa Mulungu wathu,+ m’phiri lake loyera.+ Aheberi 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma m’malomwake, inu mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda+ wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo miyandamiyanda,*+
48 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Mumzinda wa Mulungu wathu,+ m’phiri lake loyera.+
22 Koma m’malomwake, inu mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda+ wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo miyandamiyanda,*+