Nehemiya 12:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Anadutsanso pamwamba pa Chipata cha Efuraimu,+ Chipata cha Mzinda Wakale,+ Chipata cha Nsomba+ mpaka kukafika pa Nsanja ya Hananeli,+ Nsanja ya Meya+ ndi ku Chipata cha Nkhosa,+ ndipo anaima pa Chipata cha Alonda. Yesaya 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mtima wako udzalankhula motsitsa mawu+ za chinthu choopsa kuti: “Kodi mlembi ali kuti? Kodi wopereka malipiro uja ali kuti?+ Uja amawerenga nsanjayu ali kuti?”+
39 Anadutsanso pamwamba pa Chipata cha Efuraimu,+ Chipata cha Mzinda Wakale,+ Chipata cha Nsomba+ mpaka kukafika pa Nsanja ya Hananeli,+ Nsanja ya Meya+ ndi ku Chipata cha Nkhosa,+ ndipo anaima pa Chipata cha Alonda.
18 Mtima wako udzalankhula motsitsa mawu+ za chinthu choopsa kuti: “Kodi mlembi ali kuti? Kodi wopereka malipiro uja ali kuti?+ Uja amawerenga nsanjayu ali kuti?”+