Salimo 139:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ngati ndingakwere pamapiko+ a m’bandakucha,Kuti ndikakhale m’nyanja ya kutali kwambiri,+ Chivumbulutso 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma mkaziyo anapatsidwa mapiko awiri+ a chiwombankhanga chachikulu kuti aulukire kuchipululu,+ kumalo ake aja. Kumeneko n’kumene akudyetsedwa+ kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri, ndi hafu ya nthawi,+ kutali ndi njoka ija.+
9 Ngati ndingakwere pamapiko+ a m’bandakucha,Kuti ndikakhale m’nyanja ya kutali kwambiri,+ Chivumbulutso 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma mkaziyo anapatsidwa mapiko awiri+ a chiwombankhanga chachikulu kuti aulukire kuchipululu,+ kumalo ake aja. Kumeneko n’kumene akudyetsedwa+ kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri, ndi hafu ya nthawi,+ kutali ndi njoka ija.+
14 Koma mkaziyo anapatsidwa mapiko awiri+ a chiwombankhanga chachikulu kuti aulukire kuchipululu,+ kumalo ake aja. Kumeneko n’kumene akudyetsedwa+ kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri, ndi hafu ya nthawi,+ kutali ndi njoka ija.+