Salimo 73:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Winanso ndani kumwambako amene ali kumbali yanga?+Palibe wina wondisangalatsa padziko lapansi koma inu nokha.+ Salimo 143:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndikupemphera nditakweza manja anga kwa inu.+Moyo wanga uli ngati dziko louma limene likulakalaka kuti muthetse ludzu lake.+ [Seʹlah.]
25 Winanso ndani kumwambako amene ali kumbali yanga?+Palibe wina wondisangalatsa padziko lapansi koma inu nokha.+
6 Ine ndikupemphera nditakweza manja anga kwa inu.+Moyo wanga uli ngati dziko louma limene likulakalaka kuti muthetse ludzu lake.+ [Seʹlah.]