Salimo 51:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Mulungu, ndilanditseni ku mlandu wa magazi,+ inu Mulungu wa chipulumutso changa,+Kuti lilime langa linene za chilungamo chanu mokondwera.+ Salimo 126:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyo tinaseka kwambiri,+Ndipo lilime lathu linatulutsa mawu okondwa.+Pamenepo anthu a mitundu ina anayamba kuuzana kuti:+“Yehova wachitira anthu amenewa zinthu zazikulu.”+
14 Inu Mulungu, ndilanditseni ku mlandu wa magazi,+ inu Mulungu wa chipulumutso changa,+Kuti lilime langa linene za chilungamo chanu mokondwera.+
2 Pa nthawiyo tinaseka kwambiri,+Ndipo lilime lathu linatulutsa mawu okondwa.+Pamenepo anthu a mitundu ina anayamba kuuzana kuti:+“Yehova wachitira anthu amenewa zinthu zazikulu.”+