Numeri 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Palibe amene walodza Yakobo,+Ngakhale kuchesa Isiraeli.+Za Yakobo ndi Isiraeli, adzati,‘Mwaonatu zimene Mulungu wachita!’+ Yoswa 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo iye anauza amunawo kuti: “Ndikudziwa kuti Yehova akupatsani ndithu dziko lino.+ Ife tagwidwa ndi mantha chifukwa cha inu,+ ndipo anthu a dziko lino ataya mtima chifukwa chokuopani.+ Nehemiya 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno adani athu onse atangomva zimenezi,+ komanso anthu a mitundu ina yotizungulira ataona, anachita manyazi ndipo anadziwa kuti ntchito imeneyi yatheka chifukwa cha Mulungu wathu.+
23 Palibe amene walodza Yakobo,+Ngakhale kuchesa Isiraeli.+Za Yakobo ndi Isiraeli, adzati,‘Mwaonatu zimene Mulungu wachita!’+
9 Ndipo iye anauza amunawo kuti: “Ndikudziwa kuti Yehova akupatsani ndithu dziko lino.+ Ife tagwidwa ndi mantha chifukwa cha inu,+ ndipo anthu a dziko lino ataya mtima chifukwa chokuopani.+
16 Ndiyeno adani athu onse atangomva zimenezi,+ komanso anthu a mitundu ina yotizungulira ataona, anachita manyazi ndipo anadziwa kuti ntchito imeneyi yatheka chifukwa cha Mulungu wathu.+