Nehemiya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sanibalati+ wa ku Beti-horoni+ ndi Tobia,+ mtumiki wachiamoni,+ atamva zimenezi anaipidwa kwambiri+ kuti kwabwera munthu wofunira ana a Isiraeli zabwino. Nehemiya 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Sanibalati,+ Tobia,+ Aluya,+ Aamoni+ ndi Aasidodi+ atamva kuti ntchito yokonza mpanda wa Yerusalemu ikupita patsogolo, pakuti malo ogumuka anali atayamba kutsekedwa, anakwiya kwambiri.
10 Sanibalati+ wa ku Beti-horoni+ ndi Tobia,+ mtumiki wachiamoni,+ atamva zimenezi anaipidwa kwambiri+ kuti kwabwera munthu wofunira ana a Isiraeli zabwino.
7 Ndiyeno Sanibalati,+ Tobia,+ Aluya,+ Aamoni+ ndi Aasidodi+ atamva kuti ntchito yokonza mpanda wa Yerusalemu ikupita patsogolo, pakuti malo ogumuka anali atayamba kutsekedwa, anakwiya kwambiri.