Yobu 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye waika abale anga enieni kutali ndi ine,+Ndipo ngakhale anthu ondidziwa andisiya. Salimo 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndakhala chitonzo+ pamaso pa onse odana nane,+Ndipo kwa anthu oyandikana nawo ndakhala chitonzo chachikulu,+Kwa anthu ondidziwa ndakhala woopsa.+Akandiona ndili panja amandithawa.+ Mateyu 26:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Koma zonsezi zachitika kuti malemba a aneneri akwaniritsidwe.”+ Kenako ophunzira ake onse anamuthawa, n’kumusiya yekha.+ Yohane 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anabwera kudziko lakwawo, koma anthu akwawo enieniwo sanamulandire.+ Yohane 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Abale akewo+ sanali kumukhulupirira.+
11 Ndakhala chitonzo+ pamaso pa onse odana nane,+Ndipo kwa anthu oyandikana nawo ndakhala chitonzo chachikulu,+Kwa anthu ondidziwa ndakhala woopsa.+Akandiona ndili panja amandithawa.+
56 Koma zonsezi zachitika kuti malemba a aneneri akwaniritsidwe.”+ Kenako ophunzira ake onse anamuthawa, n’kumusiya yekha.+