Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 28:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kumeneko kunali mneneri wa Yehova dzina lake Odedi. Iye anapita kukakumana ndi asilikali omwe anali kubwerera ku Samariya n’kuwauza kuti: “Tamverani! Yehova Mulungu wa makolo anu wapereka Ayuda m’manja mwanu chifukwa chakuti anawakwiyira kwambiri.+ N’chifukwa chake inuyo mwapha anthu pakati pawo mwaukali kwambiri,+ ndipo ukaliwo wafika mpaka kumwamba.+

  • Salimo 109:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Chifukwa chakuti sanakumbukire kusonyeza kukoma mtima kosatha,+

      M’malomwake anapitiriza kuthamangitsa wosautsika ndi wosauka,+

      Komanso munthu wa mtima wachisoni kuti amuphe.+

  • Yesaya 53:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Zoonadi, iye anatinyamulira matenda athu+ ndipo anatisenzera zowawa zathu.+ Koma ifeyo tinamuona ngati wosautsidwa,+ wokwapulidwa ndi Mulungu,+ ndiponso wozunzidwa.+

  • Zekariya 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndakwiyira kwambiri anthu a mitundu ina amene akukhala mwabata.+ Ndawakwiyira chifukwa chakuti ine ndinangokwiyira anthu anga pang’ono pokha,+ koma anthu amenewa anakulitsa tsoka la anthu angawo.”’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena