Deuteronomo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti ndi mtundu winanso uti wamphamvu+ umene milungu yake ili pafupi nawo, monga mmene Yehova Mulungu wathu alili pafupi ndi ife, tikamaitanira pa iye+ nthawi zonse? 2 Mbiri 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nyumba imene ndikumangayi idzakhala yogometsa,+ pakuti Mulungu wathu ndi wamkulu kuposa milungu ina yonse.+
7 Pakuti ndi mtundu winanso uti wamphamvu+ umene milungu yake ili pafupi nawo, monga mmene Yehova Mulungu wathu alili pafupi ndi ife, tikamaitanira pa iye+ nthawi zonse?
5 Nyumba imene ndikumangayi idzakhala yogometsa,+ pakuti Mulungu wathu ndi wamkulu kuposa milungu ina yonse.+