Ekisodo 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo Mose anatambasula dzanja lake ndi kuloza kumwamba ndi ndodo yake. Atatero, Yehova anachititsa mabingu ndipo anagwetsa matalala+ ndi moto padziko lapansi. Choncho Yehova anapitiriza kugwetsa matalala padziko la Iguputo. Salimo 105:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Anawagwetsera matalala m’malo mwa mvula,+Anawagwetseranso moto woyaka, walawilawi m’dziko lawo.+
23 Ndipo Mose anatambasula dzanja lake ndi kuloza kumwamba ndi ndodo yake. Atatero, Yehova anachititsa mabingu ndipo anagwetsa matalala+ ndi moto padziko lapansi. Choncho Yehova anapitiriza kugwetsa matalala padziko la Iguputo.