Ekisodo 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo Mose anatambasula dzanja lake ndi kuloza kumwamba ndi ndodo yake. Atatero, Yehova anachititsa mabingu ndipo anagwetsa matalala+ ndi moto padziko lapansi. Choncho Yehova anapitiriza kugwetsa matalala padziko la Iguputo. Yobu 38:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zimene ndazisungira nthawi ya zowawa,Ndi tsiku lomenyana komanso lankhondo?+ Salimo 78:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Anapha mitengo yawo ya mpesa ndi mvula yamatalala.+Anapha mitengo yawo ya mkuyu ndi matalala.+
23 Ndipo Mose anatambasula dzanja lake ndi kuloza kumwamba ndi ndodo yake. Atatero, Yehova anachititsa mabingu ndipo anagwetsa matalala+ ndi moto padziko lapansi. Choncho Yehova anapitiriza kugwetsa matalala padziko la Iguputo.