Ekisodo 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu adzamva+ ndipo adzatekeseka.+Okhala ku Filisitiya adzamva zopweteka ngati za pobereka.+ Salimo 60:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mowabu ndi beseni langa losambiramo.+Ndidzaponyera Edomu nsapato zanga.+Ndidzafuula mosangalala chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+
8 Mowabu ndi beseni langa losambiramo.+Ndidzaponyera Edomu nsapato zanga.+Ndidzafuula mosangalala chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+