Yobu 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Masiku a moyo wako+ adzakhala owala kuposa masana.Usiku udzakhala ngati m’mawa.+ Yeremiya 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anakonzekera kumuthira nkhondo ndipo anati:+ “Nyamukani, tiyeni tipite dzuwa lili paliwombo!”+ “Tsoka ife chifukwa nthawi yatithera ndipo zithunzithunzi zikupitiriza kutalika!” Yeremiya 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Akazi awo amasiye achuluka kwambiri pamaso panga kuposa mchenga wa kunyanja. Ndibweretsa wowononga kwa mayi ndi mnyamata, dzuwa lili paliwombo.+ Ndiwachititsa kugwidwa ndi mantha ndi kuwasokoneza mwadzidzidzi.+ Yeremiya 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Munthu ameneyo akhale ngati mizinda imene Yehova waigonjetsa popanda kuimvera chisoni.+ M’mawa kwambiri azimva kulira kofuula ndipo masana azimva chizindikiro chochenjeza.+
4 Anakonzekera kumuthira nkhondo ndipo anati:+ “Nyamukani, tiyeni tipite dzuwa lili paliwombo!”+ “Tsoka ife chifukwa nthawi yatithera ndipo zithunzithunzi zikupitiriza kutalika!”
8 Akazi awo amasiye achuluka kwambiri pamaso panga kuposa mchenga wa kunyanja. Ndibweretsa wowononga kwa mayi ndi mnyamata, dzuwa lili paliwombo.+ Ndiwachititsa kugwidwa ndi mantha ndi kuwasokoneza mwadzidzidzi.+
16 Munthu ameneyo akhale ngati mizinda imene Yehova waigonjetsa popanda kuimvera chisoni.+ M’mawa kwambiri azimva kulira kofuula ndipo masana azimva chizindikiro chochenjeza.+