Salimo 39:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani! Mwachepetsa masiku anga.+Ndipo nthawi ya moyo wanga si kanthu pamaso panu.+Ndithudi, munthu aliyense ngakhale atakhala wamphamvu bwanji, sali kanthu koma ali ngati mpweya wotuluka m’mphuno.+ [Seʹlah.] Salimo 89:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Kumbukirani utali wa moyo wanga.+Kodi ana onse a anthu munawalenga pachabe?+
5 Taonani! Mwachepetsa masiku anga.+Ndipo nthawi ya moyo wanga si kanthu pamaso panu.+Ndithudi, munthu aliyense ngakhale atakhala wamphamvu bwanji, sali kanthu koma ali ngati mpweya wotuluka m’mphuno.+ [Seʹlah.]