Salimo 112:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Waunika mu mdima kuti anthu owongoka mtima aone kuwala.+ ח [Chehth]Iye ndi wachisomo, wachifundo ndi wolungama.+ Yesaya 58:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Mukatero kuwala kwanu kudzaonekera ngati m’bandakucha,+ ndipo mudzachira mofulumira kwambiri.+ Chilungamo chanu chizidzayenda patsogolo panu,+ ndipo ulemerero wa Yehova uzidzalondera kumbuyo kwanu.+
4 Waunika mu mdima kuti anthu owongoka mtima aone kuwala.+ ח [Chehth]Iye ndi wachisomo, wachifundo ndi wolungama.+
8 “Mukatero kuwala kwanu kudzaonekera ngati m’bandakucha,+ ndipo mudzachira mofulumira kwambiri.+ Chilungamo chanu chizidzayenda patsogolo panu,+ ndipo ulemerero wa Yehova uzidzalondera kumbuyo kwanu.+