Genesis 49:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dani adzakhala njoka yobisala m’mbali mwa msewu, njoka yokhala ndi tinyanga yobisala m’mphepete mwa njira, imene imaluma chidendene cha hatchi ndipo wokwerapo amagwa chagada.+ Luka 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Taonani! Inetu ndakupatsani ulamuliro kuti muzitha kupondaponda njoka+ ndi zinkhanira.+ Komanso ndakupatsani ulamuliro pa mphamvu zonse za mdani,+ ndipo palibe chimene chidzakuvulazeni.
17 Dani adzakhala njoka yobisala m’mbali mwa msewu, njoka yokhala ndi tinyanga yobisala m’mphepete mwa njira, imene imaluma chidendene cha hatchi ndipo wokwerapo amagwa chagada.+
19 Taonani! Inetu ndakupatsani ulamuliro kuti muzitha kupondaponda njoka+ ndi zinkhanira.+ Komanso ndakupatsani ulamuliro pa mphamvu zonse za mdani,+ ndipo palibe chimene chidzakuvulazeni.