Genesis 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzaika+ chidani+ pakati pa iwe+ ndi mkaziyo,+ ndi pakati pa mbewu yako+ ndi mbewu yake.+ Mbewu ya mkaziyo+ idzaphwanya mutu wako,+ ndipo iwe+ udzaivulaza chidendene.”+ Salimo 91:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Udzapondaponda mkango wamphamvu ndi njoka ya mamba,+Ndipo udzapondaponda mkango wamphamvu kwambiri ndi chinjoka.+
15 Ndidzaika+ chidani+ pakati pa iwe+ ndi mkaziyo,+ ndi pakati pa mbewu yako+ ndi mbewu yake.+ Mbewu ya mkaziyo+ idzaphwanya mutu wako,+ ndipo iwe+ udzaivulaza chidendene.”+
13 Udzapondaponda mkango wamphamvu ndi njoka ya mamba,+Ndipo udzapondaponda mkango wamphamvu kwambiri ndi chinjoka.+