Yeremiya 51:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Nebukadirezara mfumu ya Babulo wandidya.+ Wandisokoneza ndi kundisandutsa chiwiya chopanda kanthu. Wandimeza ngati chinjoka chachikulu.+ Wakhuta zinthu zanga zokoma ndipo wanditsukuluza. Chivumbulutso 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho chinjokacho+ chinaponyedwa pansi, njoka yakale ija,+ iye wotchedwa Mdyerekezi+ ndi Satana,+ amene akusocheretsa dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu. Iye anaponyedwa kudziko lapansi,+ ndipo angelo akenso anaponyedwa naye limodzi.
34 “Nebukadirezara mfumu ya Babulo wandidya.+ Wandisokoneza ndi kundisandutsa chiwiya chopanda kanthu. Wandimeza ngati chinjoka chachikulu.+ Wakhuta zinthu zanga zokoma ndipo wanditsukuluza.
9 Choncho chinjokacho+ chinaponyedwa pansi, njoka yakale ija,+ iye wotchedwa Mdyerekezi+ ndi Satana,+ amene akusocheretsa dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu. Iye anaponyedwa kudziko lapansi,+ ndipo angelo akenso anaponyedwa naye limodzi.