Yobu 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye ndiye amatiphunzitsa+ zambiri kuposa nyama zakutchire,+Ndipo amatipatsa nzeru kuposa ngakhale zolengedwa zouluka m’mlengalenga. Salimo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi wabwino ndi wolungama.+N’chifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende m’njira yoyenera.+ Yesaya 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mulungu amalangiza+ munthu moyenerera ndipo amam’phunzitsa.+ Yohane 6:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Zinalembedwa m’Mabuku a Aneneri kuti, ‘Ndipo onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine.+
11 Iye ndiye amatiphunzitsa+ zambiri kuposa nyama zakutchire,+Ndipo amatipatsa nzeru kuposa ngakhale zolengedwa zouluka m’mlengalenga.
8 Yehova ndi wabwino ndi wolungama.+N’chifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende m’njira yoyenera.+
45 Zinalembedwa m’Mabuku a Aneneri kuti, ‘Ndipo onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine.+