Salimo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Malamulo+ ochokera kwa Yehova ndi olungama,+ amasangalatsa mtima.+Chilamulo+ cha Yehova ndi choyera,+ chimatsegula maso.+ Miyambo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amapereka nzeru.+ Kudziwa zinthu ndi kuzindikira kumatuluka m’kamwa mwake.+ Yesaya 54:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+
8 Malamulo+ ochokera kwa Yehova ndi olungama,+ amasangalatsa mtima.+Chilamulo+ cha Yehova ndi choyera,+ chimatsegula maso.+
13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+