Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 40:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chilungamo chanu sindinachibise mumtima mwanga.+

      Ndinalengeza za kukhulupirika kwanu ndi chipulumutso chanu.+

      Sindinabise kukoma mtima kwanu kosatha ndi choonadi chanu mumpingo waukulu.”+

  • Salimo 71:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakamwa panga padzanena za chilungamo chanu,+

      Padzanena za chipulumutso chanu tsiku lonse,+

      Pakuti ntchito za chilungamo ndi chipulumutso chanu ndi zochuluka ndipo sindinathe kuziwerenga.+

  • Yesaya 52:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mapazi+ a munthu yemwe akuyenda pamwamba pa mapiri pobweretsa uthenga wabwino, ndi okongola kwabasi!+ Munthu yemwe akulengeza za mtendere,+ yemwe akubweretsa uthenga wabwino wa zinthu zabwino kuposa kale,+ yemwe akulengeza za chipulumutso,+ yemwe akuuza Ziyoni kuti: “Mulungu wako wakhala mfumu.”+

  • Machitidwe 13:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Amuna inu, abale anga, inu ana a mbadwa za Abulahamu, ndi ena onse oopa Mulungu amene ali pakati panu, mawu a chipulumutso chimenechi atumizidwa kwa ife.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena