Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 16:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Nthawi yomweyo anthuwo anachoka kumbali zonse za mahema a Kora, Datani ndi Abiramu. Zitatero, Datani ndi Abiramu anatuluka n’kuima pamakomo a mahema awo,+ limodzi ndi akazi awo, ana awo.

  • Numeri 26:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Zitatero, nthaka inayasama n’kuwameza.+ Koma Kora anafa pamene moto unanyeketsa gulu la amuna 250.+ Choncho iwowa anakhala chitsanzo chopereka chenjezo.+

  • Deuteronomo 11:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 kapena zimene anachitira Datani ndi Abiramu,+ ana a Eliyabu, mwana wa Rubeni, pamene dziko linatsegula pakamwa pake ndi kuwameza pamodzi ndi mabanja awo, mahema awo, ndi chamoyo china chilichonse chimene chinali pakati pawo. Dziko linawameza ali pakati pa Aisiraeli onse).+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena