Numeri 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Kora+ mwana wa Izara,+ mwana wa Kohati,+ mwana wa Levi,+ anagwirizana ndi adzukulu a Rubeni,+ omwe ndi Datani+ ndi Abiramu+ ana a Eliyabu,+ komanso Oni mwana wa Pelete, kuti aukire. Salimo 106:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo dziko lapansi linatseguka ndipo linameza Datani,+Ndi kufotsera msonkhano wa Abiramu.+
16 Tsopano Kora+ mwana wa Izara,+ mwana wa Kohati,+ mwana wa Levi,+ anagwirizana ndi adzukulu a Rubeni,+ omwe ndi Datani+ ndi Abiramu+ ana a Eliyabu,+ komanso Oni mwana wa Pelete, kuti aukire.