Levitiko 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukupitikitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja,+ ndipo mizinda yanu idzawonongedwa ndi kukhala mabwinja. Salimo 44:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwatipereka kwa adani athu kuti atidye ngati nkhosa,+Ndipo mwatimwaza pakati pa anthu a mitundu ina.+ Ezekieli 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komanso ndinakweza dzanja langa powalumbirira m’chipululu,+ kuti ndidzawabalalitsira ku mitundu ya anthu ndi kuwamwazira m’mayiko osiyanasiyana,+
33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukupitikitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja,+ ndipo mizinda yanu idzawonongedwa ndi kukhala mabwinja.
11 Mwatipereka kwa adani athu kuti atidye ngati nkhosa,+Ndipo mwatimwaza pakati pa anthu a mitundu ina.+
23 Komanso ndinakweza dzanja langa powalumbirira m’chipululu,+ kuti ndidzawabalalitsira ku mitundu ya anthu ndi kuwamwazira m’mayiko osiyanasiyana,+