Oweruza 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anasiya Yehova, Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa m’dziko la Iguputo,+ n’kuyamba kutsatira milungu ina mwa milungu ya anthu owazungulira.+ Anayamba kugwadira milungu imeneyo, moti anakhumudwitsa Yehova.+ 2 Mafumu 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anapitiriza kutumikira mafano onyansa.*+ Ponena za mafano amenewa, Yehova anawauza kuti: “Musachite zimenezi.”+ Hoseya 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Efuraimu wagwirizana ndi mafano.+ Musiyeni aona!+
12 Iwo anasiya Yehova, Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa m’dziko la Iguputo,+ n’kuyamba kutsatira milungu ina mwa milungu ya anthu owazungulira.+ Anayamba kugwadira milungu imeneyo, moti anakhumudwitsa Yehova.+
12 Anapitiriza kutumikira mafano onyansa.*+ Ponena za mafano amenewa, Yehova anawauza kuti: “Musachite zimenezi.”+