1 Mafumu 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba,+ ngakhale kumwambamwamba,+ simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba+ imene ndamangayi? Salimo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,+Inuyo ulemerero wanu ukusimbidwa kumwambamwamba!+
27 “Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba,+ ngakhale kumwambamwamba,+ simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba+ imene ndamangayi?
8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,+Inuyo ulemerero wanu ukusimbidwa kumwambamwamba!+