Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+

      Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+

      Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+

  • Salimo 89:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Pakuti ndani kumwamba angayerekezeredwe ndi Yehova?+

      Ndani angafanane ndi Yehova pakati pa ana a Mulungu?+

  • Yesaya 36:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ngati inu mungandiuze kuti, ‘Tikudalira Yehova Mulungu wathu,’ kodi si iye amene Hezekiya wamuchotsera malo ake okwezeka+ ndi maguwa ake ansembe,+ n’kuuza Yuda ndi Yerusalemu kuti, ‘Muzigwada pamaso pa guwa lansembe ili’?”’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena